fbpx

Zikomo Foundation imaonetsetsa kuti  kusintha kubwere m’dziko potenga nawo mbali mu zinthu zogwirika. Ngati inu mukufuna kutenga nawo gawo, pali njira zingapo zokhazikika zimene mungatsate kuti mutithandize:

Icon_Freiwilligenarbeitleisten
Kugwira ntchito mongodzipereka

Modzipereka mukhoza kugwira nafe ntchito mumagawo osiyanasiyana. Mukudzipereka kwanu mukhoza kubweretsa kusintha mu miyoyo ya ana ochuluka ku Malawi.

 Tipezeni!

Icon_Botschafterwerden
Kukhala otiyimilira

Auzeni anzanu za ntchito imene Zikomo Foundation ikugwira. Izi zithandiza kupititsa patsogolo ntchito zathu. Tithandizana, ingotifikirani.

Tipezeni!

Icon_Finanziellunterstutzen
Othandiza

Zikomo chifukwa cha thandizo lanu la zachuma lomwe litipatse kuthekera kofikira ana ambiri, kuthandiza ntchito zathu komanso kuyambitsa zatsopano.

Perekani tsopano

Icon_Netzwerkeschaffen
Maubale a ntchito

Tidziwitseni za maganizo anu pofuna kugwira nafe ntchito zotukula miyoyo ya wanthu.

Tipezeni!