fbpx

Zikomo Foundation imagwira ntchito yake mosabisa kalikonse. Ndondomeko ya zachuma imaonedwa ndi kuunguzidwa ndi akatswiri a kauniuni wa zachuma oyima pa okha. Izi zimatithandizira kutsatira ndondomeko zonse zoyenera.

Ndondomeko ya ndalama chaka cha 2016

Ripoti la akatswiri a kauniuni wa chaka cha 2016

Ndondomeko ya ndalama chaka cha 2015

Ripoti la akatswiri a kauniuni wa chaka cha 2015